We
are
redeemed,
glory
to
the
Lamb!
Yes
Lord,
we
stand
in
Your
light
today.
Ndipereka
zanga
zonse
Mwaufulu
kwa
Yesu;
Ndidzamkonda
kopambana,
Tsiku
lili
lonsetu.
Ndiperekatu
Zonse
kwa
Yesu;
Ndipereka
zonse
kwa
'Nu,
Dalitseni. 2
Ndipereka
zanga
zonse
Pamapazi
a
Yesu;
Zapadziko
ndazikana,
Nditengeni
Yesu
'Nu.
Ndiperekatu
Zonse
kwa
Yesu;
Ndipereka
zonse
kwa
'Nu,
Dalitseni.
Ndipereka
zanga
zonse,
Ndipo
n'khale
wanutu;
Mzimu
wanu
'ndidziwitse
Kuti
ndine
wanudi.
Ndipereka
zanga
zonse,
Ndili
wanu
ndense
'ne;
Nditamanda
Dzina
lanu,
Aleluya,
Ambuye.
Ndiperekatu
Zonse
kwa
Yesu;
Ndipereka
zonse
kwa
'Nu,
Dalitseni.
Kwathu
sipadziko,
ndingopitirira,
Ndadzikundikira
chuma
Kumwambako;
Mngelo
akodola
pakhomo
la
m'mwamba;
Ndipo
dziko
lapansi
sindyesa
kwathu.
Mbuye
ndinu
bwenzi
langa
ndithu,
Ndichitenji
ngati
Kumwamba
sikwathu?
Mngelo
akodola
pakhomo
la
m'Mwamba,
Ndipo
dziko
lapansi
sindiyesa
kwathu.
Andiyembekeza,
chinthuchi
ndidziwa,
Mpulumutsi
wanga
wandikhulukira;
Adzandipyoletsa
pamene
ndafoka;
Ndipo
dziko
lapansi
sindiyesa
kwathu.
Mayi
watsogola
ku
Ulemerero,
Ndifuna
kugwira
dzanja
lake
konko,
Andidikiranso
pakhomo
la'Mwamba;
Ndipo
dziko
lapansi
sindiyesa
kwathu.
Mu
ulemerero
tidzakhala
m'yaya,
Oyera
mtimawo
ali
kulamira;
Ati, "
Aleluya
kwa
Mlungu
Wamphamvu."
Ndipo
dziko
lapansi
sindiyesa
kwathu.
Ambiri
tikondwera
mwa
Yesu,
Nanga
inu?
Nanga
inu?
Tapeza
chipulumutso
ndithu;
Nanga
inu?
Nanga
inu?
Masiku
onse
timakondwera
Pakumva
Mawu
ake
a
Yesu;
Wolalikira
tidzamumvera;
Nanga
inu?
Nanga
inu?
Ife
tiyembekezera
Yesu,
Nanga
inu?
Nanga
inu?
Chimwemwecho
chili
mumtimamu;
Nanga
inu?
Masiku
onse
timakondwera
Pakumva
Mawu
ake
a
Yesu;
Wolalikira
tidzamumvera;
Nanga
inu?
Nanga
inu?
Titasokera
tinabwerera,
Nanga
inu?
Nanga
inu?
Tadziwa
kuti
ndiwo
uchimo;
Nanga
inu?
Masiku
onse
timakondwera
Pakumva
Mawu
ake
a
Yesu;
Wolalikira
tidzamumvera;
Nanga
inu?
Nanga
inu?
Tinachoka
munjira
ya
imfa,
Nanga
inu?
Nanga
inu?
Takopeka
ndi
Mawu
a
Yesu;
Nanga
inu?
Masiku
onse
timakondwera
Pakumva
Mawu
ake
a
Yesu;
Wolalikira
tidzamumvera;
Nanga
inu?
Nanga
inu?
Kuli
dziko
labwino
m'Mwamba
Lakuwala
koposa
dzuwa;
Yesu
atikonzera
malo
Pokhalira
ife
komweko.
Bwinoli
tipita,
Tikumana
mwa
Dziko
lija,
Bwinoli
tipita,
Tikumana
mwa
Dziko
lija.
Tidzimba
komweko
nyimbo
Za
abwino
omvera
Yesu,
Sitidzamva
chisoni
ife,
Tidzakondwa
masiku
onse.
Bwinoli
tipita,
Tikumana
mwa
Dziko
lija,
Bwinoli
tipita,
Tikumana
mwa
Dziko
lija
Tidzatama
Atate
wathu
Kuti
Iye
'napatsa
Yesu
Kuchotsera
zochimwa
zonse,
Ndi
kutidalitsira
ife.
Bwinoli
tipita,
Tikumana
mwa
Dziko
lija,
Bwinoli
tipita,
Tikumana
mwa
Dziko
lija
Ndine
Mbusayo
wabwino,
Ndinafera
nkhosazo;
Yotayika
ndaifuna,
Mpaka
ndataya
moyo.
Mbulu
wanding'amba
m'nthiti,
Wanding'ambanso
m'manja,
Wanding'ambira
zobvala,
Ndatsala
waumphamwi.
Nkhosa
zanga
zimandimva
Ndikaziitanazo;
Ndimazipatsa
moyowo,
Atate
nazisunga.
Mbulu
wanding'amba
m'nthiti,
Wanding'ambanso
m'manja,
Wanding'ambira
zobvala,
Ndatsala
waumphamwi.
M'kati
ali
fisiyo;
Musanyengedwa
anthuni,
Ine
ndine
Mbusayo.
Mbulu
wanding'amba
m'nthiti,
Wanding'ambanso
m'manja,
Wanding'ambira
zobvala,
Ndatsala
waumphamwi.