Frobits
🎵 A song made on Frobits

Heart of the Master (Remix)

0:000:00
Download
Reply with a song
Lyrics

[male

vocals] 1

Ndikonda

Mlungu

pomva

Mbuye

wanga

Amva

pemphero

ndi

kulira

kwanga,

Namatchereza

khutu

nditapfuula,

Andithandiza,

nandipulumutsa. 2

Mulungu

wanga

ndiye

wachifundo

Ndiwolungama

mtima

ndi

wabwino;

Apulumutsa

anthu

akufoka,

Akathandiza

nkhawa

imachoka. 3

Mtimanga,

bwera

kuti

upumule,

Wakuchitiranso

zokoma

Mbuye,

Wakuchotsera

imfa

ndi

misozi,

Ndingakhumudwe

asungira

phazi. 4

Nditani

ine

kubwezera

Mbuye

Zokoma

zonse

anandichitira?

Chipulumutso

chake

ndidzatama,

Ndinalumbira

zija

ndidzapatsa. 5

Imfa

ya

anthu

ake

imkomera,

Awalandira

m'nyumba

zokonzeka,

Mbuye,

kapolo

wanu

ndipereka

Nsembeyi

yonga

yanu,

ndine

ndekha.

More songs by israel Listen to songs created by others
FROBITS