Yeah, yeah
Ndi uyu munthu mmodzi
Zikubwera, kumvera, kukhulupirira
Taona, tamvetsetsa
Chikondi nichofunika pa munthu aliyense
Koma nthawi zina ife timachisiya kuthawa
Mtima ukupweteka tikayenda tokha
Chikondi chija chimasowa m’moyo mwathu
Tikufuna mtendere koma timayiwala
Kuti chikondi ndiye njira yoyenera
Tikufunafuna zinthu zopanda pake
Pamene chikondi chimakhala pafupi nafe
Nanga why timachisiya, chikondi ichi?
Nanga why timachisiya, chikondi ichi?
Nanga why timachisiya, chikondi ichi?
Nanga why timachisiya, chikondi ichi?
Chikhulupiriro nichofunika aliyense
Nanga why timachisiya, nanga why?
Tikamadzimva otaya mtima m’njira
Tikuyenera kuyang’ana kumwamba
Chikhulupiriro ndicho nyali m’mdima
Chimatipatsa mphamvu yakulimbana
Koma nanga why timachisiya, kusiya?
Tikuyenda m’manja mwa Mulungu yekha
Nanga why timachisiya, chikondi ichi?
Nanga why timachisiya, chikondi ichi?
Nanga why timachisiya, chikondi ichi?
Nanga why timachisiya, chikondi ichi?
Kuwerenga mawu akulimbikitsa
Kuti tikhale okonzeka mtima
Kuplikila nikofunika aliyense
Nanga why timakusiya Mulungu?
Ooh, musasiye, musasiye
Lero ndilo tsiku losinthira
Mulungu ali nafe, samatisiya ayi
Ife ndife timachoka m’njira yake
Koma chikondi chimabwerera mtima
Chikhulupiriro chimalimba m’miyoyo
Tiye tiyambe lero ndi mtima watsopano
Kusiyana ndi zonse zimene zinali zoipa
Tikulira, tikupempha, tikuyembekezera
Kuti chikondi chikhale m’mitima mwathu
Nanga why timachisiya, chikondi ichi?
Nanga why timachisiya, chikondi ichi?
Nanga why timachisiya, chikondi ichi?
Nanga why timachisiya, chikondi ichi?
Nanga why, nanga why?
Musasiye Mulungu
Chikondi nichofunika
Zikomo, chikhulupiriro chikhale nafe
Yeah, mwa munthu mmodzi
Tikuyenda limodzi
Chikondi chigonjetse zonse
Yeah, nanga why?