[male vocals] Yaaaa
eye,
Eeee
Naadi
pano!
PS
ONE
MAN
MJDC-Goma,
listen
now.
Ine
ninkhala
mutu
umababa,
why?
Because
I
love
you,
my
baby.
Ine
ninkhala
mutu
umababa,
why?
I
love
you,
my
sunshine,
my
lady.
Manje,
why
umanichokamo
Baby?
Umanichokamo
why?
Bebe.
Umanichokamo,
umandisiya
ndekha.
Ndimamva
ngati
dziko
likupindika.
Ine
ninkhala
mutu
umababa,
why?
I
love
you!
Ine
ninkhala
mutu
umababa,
why?
I
love
you!
Manje
why,
umanichokamo?
Baby,
umanichokamo
Bebe
aaaa.
Yaaa
leka
nikuuze,
I
PS
ONE
MAN
MJDC-Goma.
Ine
nimakunda
ngati
bingiza
namavi,
E
e,
ine
nimakunda
monga
mata
nalulimi,
Ya,
ya,
ine
nimakunda
monga
mbowowo
nakutu,
Baby
nimakunda
monga
meso
namisozi.
Thatβ
s
why
Iβ
m
saying,
listen
baby.
Ine
ninkhala
mutu
umababa,
why?
I
love
you!
Ine
ninkhala
mutu
umababa,
why?
I
love
you!
Manje
why,
umanichokamo?
Baby,
umanichokamo
Bebe
aaaa.
Mmm,
baby,
come
here.
Musandichokere,
ndikufuna
iwe.
Mtima
wanga
umangogunda
chifukwa
cha
iwe.
Ine
ndine
wako,
iwe
ndiwe
wanga.
Nthawi
zonse,
m'mawa
mpaka
madzulo.
Ine
ninkhala
mutu
umababa,
why?
Because
I
love
you,
mmmm.
Nkhawa
zikuchulukira,
baby
come
back.
Ndikufuna
kukumva
m'manja
mwanga.
Ine
nimakunda
monga
mbowowo
nakutu,
I
love
you,
oh
baby,
ndikukufuna.
Ine
ninkhala
mutu
umababa,
why?
I
love
you!
Ine
ninkhala
mutu
umababa,
why?
I
love
you!
Manje
why,
umanichokamo?
Baby,
umanichokamo
Bebe
aaaa.
I
love
you,
why,
why,
why?
Baby,
don't
leave
me,
I
need
you.
PS
ONE
MAN
MJDC-Goma,
yeah.
Ine
ninkhala
mutu
umababa,
baby,
iwe.