Frobits
🎵 A song made on Frobits

Vubwi Shadows

0:000:00
Download
Make your own song
Continues securely on the web
Lyrics

[male

vocals] *

Intro* *

Yo!

Zozwe

Ward!* *

Tikumvani!

Tikumvani!* *

Mr

Vincent

Mbewe!* *

Let's

go!*

DJ

kabs *

Hook* *

Analuzitsa

chipani

chifukwa

chosavomekeza* *

Utsogoleri

omwe

unasankhidwa* *

Mr

Vincent

Mbewe

mvera* *

Alphonso

Phiri

mvera* *

Stainly

Banda

ndi

Abulty

Sakala* *

Maxwell

mwale* *

Munawononga

chifukwa

cha

kudzikuza!*

Mr

Vincent

Mbewe

wa

Zozwe

Ward

Munkafuna

munthu

wanu

wanu

koma

Chipani

chinasankha

utsogoleri

watsopano

Iwe

unakana,

unayamba

chipongwe

Munati "

Ine

sindivomereza"

Manazonda

ma

candidates

achipani

chanu

nupita

ukasapota

otsutsa

Tsopano

chipani

chagwa

Ma

youths

akulira

chifukwa

cha

inu!

Alphonso

Phiri,

nanga

iwe

bwanji?

Unali

ndi

nzeru

koma

unayitaya

Stainly

Banda,

unali

phungu

wa

anthu

Tsopano

wakhala

mdani

wa

chipani

Munasankha

kudzikonda

Munasankha

kusagwirizana

Anthu

a

upnd

amafuna

umodzi

Inu

munabweretsa

magawano!

Abulty

Sakala,

womaliza

Iwe

ndiwe

chizindikiro

cha

kutha

Utsogoleri

unasankhidwa

ndi

anthu

Iwe

unati "

Ayi,

ine

sindikufuna"

Chifukwa

chosavomekeza

Chipani

chaluza

mavoti

Chifukwa

chosagwirizana

kwanu

azitsogoleri

Avin,

Alphonso,

abulty

sakala,

stainly

Banda

and

Maxwell

mwaleyatsala

m'mbuyo! *

Final

Hook x2* *

Analuzitsa

chipani

chifukwa

chosavomekeza* *

Utsogoleri

omwe

unasankhidwa* *

Vubwi

ifuna

atsogoleri

atsopano* *

Vubwi

ifuna

atsogoleri

atsopano* *

Osati

anthu

odzikonda!* *

Zozwe

ward,

sindemisale ,

chimphanje,

mlawe,

chisiya,

matemba,

mbande

na

vubwi

ward

dzukani!* *

Chipani

chibwerere!* *

Umodzi

ndi

mphamvu!* *

Vubwi

UPND* ---

More songs by Vmc Listen to songs created by others
FROBITS