[male
vocals] (
Acoustic
guitar
picking
with
a
slow,
swaying
rhythm) (
Soft,
mellow
fiddle
melody)
Ambiri
tikondwera
mwa
Yesu,
Nanga
inu?
Nanga
inu?
Tapeza
chipulumutso
ndithu;
Nanga
inu?
Nanga
inu?
Masiku
onse
timakondwera
Pakumva
Mawu
ake
a
Yesu;
Wolalikira
tidzamumvera;
Nanga
inu?
Nanga
inu?
Ife
tiyembekezera
Yesu,
Nanga
inu?
Nanga
inu?
Chimwemwecho
chili
mumtimamu;
Nanga
inu?
Titasokera
tinabwerera,
Nanga
inu?
Nanga
inu?
Tadziwa
kuti
ndiwo
uchimo;
Nanga
inu?
Tinachoka
munjira
ya
imfa,
Nanga
inu?
Nanga
inu?
Takopeka
ndi
Mawu
a
Yesu;
Nanga
inu?
Ufuna
kuwomboledwa
kodi?
Ilipo
mphamvu
m'mwazi
wake;
Ufuna
kugonjetsa
zoipa?
Muli
mphamvu
m'mwazi
wake.
Muli
mphamvu
yodabwitsatu
M'mwazi
wa
Yesuyo.
Muli
mphamvu
yodabwitsatu
M'mwazi
wa
Mwana
wankhosa.
Ufuna
kuleka
kunyadako?
Ilipo
mphamvu
m'mwazi
wake;
Idzatu
pa
mtanda
nutsukidwe,
Muli
mphamvu
m'mwazi
wake.
Ufuna
kuyera
kopambana?
Ilipo
mphamvu
m'mwazi
wake;
Zoipa
zonse
adzayeretsa,
Muli
mphamvu
m'mwazi
wake.
Ufuna
kugwira
ntchito
yake?
Ilipo
mphamvu
m'mwazi
wake;
Ufuna
kumuimbira
Iye?
Muli
mphamvu
m'mwazi
wake.
Ndidze
pafupi
pa
Mlungu
wanga,
Ngakhale
pamtanda
Mundikweza;
Koma
ndiimbabe,
Mbuye
mndikhalitse,
Mbuye
mndikhalitse
M'fupi
Ndinu.
Ngakhale
kuthengo
Ndasokera,
M'mdima
ndigonapa
E,
pamwala;
Koma
m'kulotako
Ndiyandikizanso
Ndiyandikizanso
M'fupi
Ndinu.
Pajapo
ndipenya
Pokwerapo,
Angelo
atsika
Kumwambako,
Ndiwo
akodola
Kuti
ndikabwere,
Kuti
ndikabwere,
M'fupi
Ndinu.
Tsono
poukanso
Wokondwatu,
Ndipeza
pomwepo
Pali
Mlungu;
Ndipo
masautso
Andisendezanso,
Andisendezanso,
M'fupi
Ndinu.
Pena
pakufadi,
N'kweza
m'Mwamba,
Dzuwa
ndi
nyenyezu
Zitsalira;
Pomwe
ndiimbanso,
Ndidza
pafupi
pa,
Ndidza
pafupi
pa
Mlungu
wanga.
Limba
mtima
mbale
wanga,
Usapunthwe
m'njirayi;
Onatu
nyenyezi
ija
Ikutsogoleradi.
Tamveratu
Mlungu
yekha,
Chita
zolungama
'we,
Yenda
bwino,
khulupirira
Mbuyeyo,
Mbuyeyo,
Ndi
kuchita
zakezi.
Taya
zako
zochenjera,
Taya
zamumdimanso;
Nthawi
zonse
khulupira,
Chita
zolungamazo.
Usayang'anire
wina
M'khondo
yako
yomweyi,
Koma
m'zonse
khulupirira
Mbuyeyo,
Mbuyeyo,
Ndi
kuchita
zakezi.
Leka
zakuipa
zako,
Myambi
yonse
yoti
bii,
Usakhulupire
mommo;
Tamveratu
Mbuyedi.
Adzadana
nawe
ena,
Ena
adzakonda
'we;
Kweza
maso,
khulupirira
Mbuyeyo,
Mbuyeyo,
Ndi
kuchita
zakezi.
Mawu
ake
atipatsa
Mphamvu
ndi
mtenderenso,
Bwino
atitsogolera,
Tikhulupirira
'wo.
Limba
mtima,
usapunthwe
M'njira
yamumdimayi;
Yenda
bwino
khulupirira
Mbuyeyo,
Mbuyeyo,
Ndi
kuchita
zakezi. (
Acoustic
guitar
fades
out
slowly)
Tapeza
chipulumutso
ndithu;... ...
Pakumva
Mawu
ake
a
Yesu; .
Ilipo
mphamvu
m'mwazi
wake; (
Acoustic
guitar
fades
out
slowly)
Tapeza
chipulumutso
ndithu;...
Nanga
inu?
Nanga
inu?
Tapeza
chipulumutso
ndithu;
Nanga
inu?
Nanga
inu? (
Acoustic
guitar
fades
out
slowly)
Tapeza
chipulumutso
ndithu;...
Nanga
inu?
Nanga
inu?
Tapeza
chipulumutso
ndithu;
Nanga
inu?
Nanga
inu?