Aweh!
Lero
ndi
tsiku
lalikulu,
happy
birthday
adadi
Mr
Ronald
mbewe!
Zikomo
Mulungu,
tisangalale
pamodzi!
Lero
kwacha
ndi
chimwemwe
chachikulu
Nyenyezi
zaonekera,
Mr
Ronald
mbewe
Dadii
Chaka
chatsopano
cha
moyo
wanu
chabwera
Tikukondwerera,
timve
ngoma
ikulira
Dziko
likuvina
chifukwa
imwe
mulipo
Timamva
kunyada,
Atate
happy
birthday
happy
birthday,
lero
ndi
tsiku
lamu
losangalalaa
Tamwera,
tivine,
tiyimbire
dzina
Mr
Ronald
mbewe,
moyo
wautali
ndikufunira
mafuno
Chaka
chatsopano
ichi
chikhale
chodzaza
ndi
madalitso
Sharp
sharp,
bwerani
tonse
Atate,
lero
ndi
tsiku
lamu
lelo
na
amai
Eish,
ukula
ndithu,
mwamuna
wamphamvu
Nzeru
zikuchuluka,
moyo
ukutsekemera
Zonse
zimene
munali
kulakalaka
zichitike
Nyimbo
ikulira,
log
drum
Sangalalani
atate
pamodzi
ndi
amai,
sangalalani!
tiyeni
muyende
bwino
bwino
Happy
birthday
Ronald
mbewe,
lero
ndi
tsiku
lanu
lovina
Tamwera,
tivine,
tiyimbire
dzina
lamu
Mr
Ronald
mbewe,
moyo
wautali
ndikufunira
Chaka
chatsopano
ichi
chikhale
chodzaza
ndi
madalitso
Sharp
sharp,
bwerani
tonse
tiziphimba
lero
ndi
tsiku
lanu
mu
yanike
mulungu
pokufikizani
zaka
72
years
sichapafupi
Sho,
zikomo
atate
chifukwa
cha
zonse
Muli mphatso kwa ife tonse
Chikondi
chanu
ndi
chowona,
chili
Kondwerera,
usalole
chilichonse
kukulepheretsa
Zinthu
zikuyenda
bwino,mr
Ronald
Nthawi
yakwana
yoti
dziko
lidziwe
Kuti
ndinu
munthu
wosiyanakoo
,
tivine
ndi
Yebo,
happy
birthday
Ronald
mbewe,
ndiye
mfumu
ya
lero
popita
Happy
birthday
Mr
Ronald
mbewe,
lero
ndi
tsiku
lamu
Tamwera,
tivine,
tiyimbire
dzina
lanu
Atate,
moyo
wautali
ndikufunira
Chaka
chatsopano
ichi
chikhale
Sharp
sharp,
bwerani
tonse
tivine
Happy
72
birthday
atatee,
lero
ndi
tsiku
lanu
Nichifukwa
ife
baana
Dorothy
mbewe
amake
Martha
apunda
happy
72
birthday
mbewe
atake
fale
naeve
apunda
happy
72
birthday
atatee
Mary
mbewe
and
Janet
naeve
apunda
happy
72
birthday
Dadii
Happy
birthday
to
you
Mr
Ronald
mbewe,
zikomo,
zikomo
Tizapitirirza
kusangalala
Sho, lero ndi lachisangalalo
Happy
birthday
,
happy
birthday
to
you
dad
we
love
you
Ibrahim
Banda
iweenipataliii