(Beat +
guitar
only)
Lalalala..
Lalalala..
Niya
Rent
Siyako..
Bashi
Samu
let's
go..
Yebooo!
Nyumba
ya
rent
siyako,
olo
iwame
bwanji
siyako
Same!
Girl
uyenda
naye
siwako,
olo
awame
bwanji
siwako
Nyumba
ya
rent
siyako,
olo
ikule
bwanji
siyakooo!!!
Guy
uyenda
naye
siwako,
olo
umukonde
bwanji
siwako
Pali
munzanga
pa
Kabwata
nizibiwa!
Enzo
chita
rent
mu
nyumba
yabwino,
Anaikisa
ma
kitchen
unit,
ma
chandelier
lights!
Kwenze
kusamwa!
Paint
ku
chipupa
anachinja!
Aibala
eve
ni
tenant,
landlord
abwela...
Chokamoni
benangu
bagulaaaa!
Pali
Gelo
ine
wamene
I
know!
Enze
na
guy,
imwe
kwenze
kanthu,
Anangenesamo,
anavalikamo,
mumutima
angenamo,
Kugwilana
ma
bubuzi,
anthu
ati
ni
chikwati!
Sipanapite
nthawi,
guy
aona
ka
neighbour,
Anakwatila
na
neighbour!!!!! (
Drums
only +
log
drum +
shouting)
Siyako!
Siyako!
Iwee
manga
yako!
Munga
kondane,
munga
sekelane,
ngati
palibe
chikwati
siwako!
Akugulira
ma
gift,
na
ma
keys
ya
nyumba,
chikwati
palibe
siwako!
Mu
nga
gwilane
ma
kiss
kiss
mwaaa..
palibe
chikwati
siwako!
Dadadada..
Siyako..
Iwee
manga
yako
Niya
rent
siyako!!
Siyako.
Siyakooooo!
Ni
Bashi
Samu
pa
Chikupi!
Yebooo!