[male
vocals] (
Soft
piano
chords
swelling
into
ambient
pads)
Inu
Mulungu,
tikuyamikani;
Tibvomereza
ndinu
Ambuyathu;
Ponse,
Atate,
akugwadirani,
Ndinu
wamuyaya!
Nanu
akukuzani
amithenga,
Nanu
zam’
mwamba
ndi
zamphamvu
zake,
Nanu
angelo
a
mitundu
yonse
Akuimbirani! “
Mbuye
Woyera!
E,
Woyera
nokha!
Mbuye
Woyera!
Mbuye
wa
makamu!
Ponse
ulemu
wanu
ndi
wodzaza
Pansi
ndi
Kumwamba.”
Nanu
Atumwi
akumveka
aja,
Ndi
Aneneri
oyanjana
omwe,
Ndi
aunyinji
anakuferani
Akuyamikani.
Mpingo
woyera
wa
kwa
anthu
onse
Ukumverani,
Mfumu
ndi
Atate,
Mwana
woona
wa
ulemu
wonse,
Mzimu
Nkhoswe
yemwe.
L
Kristu
Mfumuyo
yauleme
rero!
Mwana
wosatha
wa
Atate
ndinu!
Simunanyoza
mimba
ya
namwali
Potipulumutsa.
Imfa
mutagonjetsa
ndi
zowawa,
Njira
munatsegula
tikalowe
Momwe
mukhala
Inu
ndi
Atate
Mwaulemerero.
Kumva
milandu
yathu
mudzabwera
Mutithandize,
atumiki
anu;
Mwatiwombola
nawo
mwazi
wanu:
Mutipulumutse
Mtiwerengere
mMwamba
ndi
oyera;
Mutidalitse,
ndife
anthu
anu;
Moyo
wosatha
mutipatse
tonse,
Mutilamulire.
Tsiku
ndi
tsiku
timalemekeza;
Nanu
tikukuzani
osaleka;
Mbuye,
mtisunge
tingachimwe
lero:
Mtichitire
nsisi.
Mbuye,
chifundo
chanu
chitigwere
Monga
tikhulupira
Inu
nokha;
Ndakhulupira
zedi
mwanu,
Mbuye,
Ndisagome
konse!
Ndi
Aleluya
imbirani
'Tate
wathu,,
Analenga
zonse.
Chifundo
chake
chachikulu,
Nzeru,
mphamvu
ndi
ufumu
Tiyamike
tonse.
Ndi
Aleluya
imbirani
Yesu
Khristu
Mpulumutsi,
Anachoka
kwawo,
Nakhala
munthu,
pansi
pano,
Nasauka,
natifera,
Natisiyira
mawu.
Ndi
Aleluya
imbirani
Mzimu
wake
Wakuyera,
Amakhala
nafe.
Atilangiza
za
Mulungu,
Nayeretsanso
mitima
Ya
akhristu
ife.
Mulungu
wathu
tiyamika,
'Tate,
Mwana,
Mzimu
yemwe
Aleluya
Inu.
Woyera
Inu
ndi
wamphamvu,
Muyenera
anthu
onse
Agwadire
Inu.
Munthu
Wazisoniyo
Timtcha
dzina
lakelo,
Mpulumutsi
linanso;
Aleluya,
ndiye
Yesu.
Anapeputsidwako,
Nandifera
m'mtandamo,
Anandiwombolayo;
Aleluya,
ndiye
Yesu.
Ife
tinachimwadi,
Iye
sanachimwa
'yi,
Anachotsa
tchimoli,
Aleluya,
ndiye
Yesu.
Anapachikidwatu,
Natha
ntchito
yake
myu!
Anakwera
m'Mwamba
duu!
Aleluya,
ndiye
Yesu.
Adzabwera
Iyenso
Kudzatenga
akewo;
Nyimbo
tidzaimbanso,
Aleluya,
ndiye
Yesu.
Ooh,
we
lift
You
up
You
are
the
everlasting
King
We
bow
before
Your
throne (
Fading
piano
and
strings)
Amen.