Frobits
🎵 A song made on Frobits

Chikulupililo Cha Mai

0:000:00
Download
Reply with a song
Lyrics

Mverani

bwino…

bwino

Iyi

nkhani

ndikukufotokoza…

Ine

Prophetic

Professor

Fizwell…

Nkhani

ya

mayi

wolimba

mtima…

Zina

Lake

ni

Linet

Mwanza…

Ndi

nkhani

ya

mayi,

dzina

lake

Linet

Anali

ndi

banja,

moyo

unali

bwino

Koma

tsiku

lina,

imfa

inabwera

Mwamuna

wake

anamusiya

ndi

ana

atatu

Anyamata

okha

okha,

moyo

unavuta

Misozi

ndi

Mavuto,

tsiku

ndi

tsiku

Koma

sanasiye,

anaimirira

yekha

Kukhala

mayi

ndi

Tate

Panthawi

imodzi

Chikhulupiriro

cha

mayi,

sichisila

yayi

Mulungu

amaona,

amam’

teteza

Chikhulupiriro

cha

mayi,

sichisila

yayi

Mulungu

amaona,

amam’

teteza

Patapita

nthawi,

zaka

zitatu

Anakumana

ndi

bwenzi

lakale

Anapatsa

mtima

wake

mwayi

wachiwiri

Kukhulupirira

moyo

uzachinja

Anakwatirana,

na

ana

ena

anabwera

Banja

linakula,

chiyembekezo

chabwera

Koma

zaka

zili

four

pamene

zinafika

Mwamuna

anapondoka…

anasiya

banja

Anatsala

yekha

ndi

ana

ambiri

Zinakhala

zolemetsa

kuchila

kudala

Koma

mayi

ameneyo

sanagwe

pansi

Anapitiriza

kulimbikira

moyo

Chikhulupiriro

cha

mayi,

sichisila

yayi

Mulungu

amaona,

amam’

teteza

Chikhulupiriro

cha

mayi,

sichisila

yayi

Mulungu

amaona,

amam’

teteza

Umoyo

unaleta,

mayesero

ambiri

Anataya

mwana

wake,

Omega,

infa

Yatenga

Ululu

waukulu,

mtima

unalira

Koma

sanasiye

baana

Banasala

bake

Anatsala

ndi

ana

asanu

ndi

mmodzi

mtsikana

Ngakhale

Mabvuto

yanali

yakulu

Chikhulupiriro

chake

chinakhalabe

cholimba

Anapitiriza

kuyenda

ndi

Mulungu

Wake

Chikhulupiriro

cha

mayi,

sichisila

yayi

Mulungu

amaona,

amam’

teteza

Chikhulupiriro

cha

mayi,

sichisila

yayi

Mulungu

amaona,

amam’

teteza

Ankagwira

ntchito,

usiku

ndi

Kuseni

Nthawi

zina

ankakhala

opanda

pokhala

Koma

sanasiye,

anakhulupirira

Mulungu

Pang’

ono

ndi

pang’

ono

zinthu

zinasintha

Anamanga

nyumba,

ndi

manja

ake

Kuchokera

pa

kusowa

kufika

pa

kukhala

Banja

silinathandize,

anali

yekha

Koma

Mulungu

anali

naye

nthawi

zonse

Lero

madalitso

akuonekera

Kupyolera

mubana

bake

Mayi

ameneyo

ndi

survivor

Ndipo

ndi

winner

weni-weni

Chikhulupiriro

cha

mayi,

sichisila

yayi

Mulungu

amaona,

amam’

teteza

Chikhulupiriro

cha

mayi,

sichisila

yayi

Mulungu

amaona,

amam’

teteza

Iyi

ndi

nkhani

ya

Linet

Mwanza…

Mayi

wolimba

Chikhulupiriro …

Ine

Prophetic

Professor

Fizwell…

ndikukuuza…

Ngakhale

moyo

uli

wovuta…

Musasiye…

Chifukwa

Mulungu

amaona…

More songs by Professor Listen to songs created by others
FROBITS