Frobits
🎵 A song made on Frobits

Vubwi Moving Forward

0:000:00
Download
Make your own song
Continues securely on the web
Lyrics

[male vocals] Intro*

Yo!

Vubwi

Constituency!

Zozwe

Ward

tiyeni

tiyimbe!

Ndale

za 2026! *

Hook*

Analuzitsa

chipani

ku

Vubwi

Chifukwa

chosavomekeza

utsogoleri

Utsogoleri

omwe

unasankhidwa

ndi

anthu

Tsopano

akuuza

anthu

Tonse

Alliance!

Mr

Vincent

Mbewe

wa

Zozwe

Unali

mkulu

mu

chipani

Utsogoleri

utasintha

Iwe

unakana

kuvomereza

Unayamba

kuyendayenda

Kuuza

anthu "

Musavote

UPND" "

Voterani

Tonse

Alliance"

Vubwi

yagwa

chifukwa

cha

iwe!

Alphonso

Phiri,

Stainly

Banda

Munalowa

mu

gulu

la

magawano

M'malo

molimbikitsa

umodzi

Munagawikana

chipani

Anthu

a

Vubwi

amafuna

chitukuko

Inu

mubweretsa

mikangano

Chipani

chomwe

chinamanga

Vubwi

Tsopano

chili

pansi

chifukwa

cha

inu! *

Verse 3 -

Abulty

Sakala*

Abulty

Sakala

nayenso

Analowa

mu

Tonse

Alliance

campaign

Abulty

Sakala

nayenso

Analowa

mu

Tonse

Alliance

campaign

Anthu

amadabwa

Kodi

mfundo

zili

kuti?

Ngati

simukugwirizana

ndi

utsogoleri

Bwerani

patebulo

tikambirane

Osati

kugulitsa

Vubwi

Ku

Tonse

Alliance!

Osati

kugulitsa

Vubwi

Ku

Tonse

Alliance! *

Outro

Hook*

Vubwi

ifuna

umodzi!

Zozwe

ifuna

umodzi!

Siyani

magawano!

Bweretsani

chipani! *

Outro

Hook*

Vubwi

ifuna

umodzi!

Zozwe

ifuna

umodzi!

Siyani

magawano!

Bweretsani

chipani! ---

More songs by Vmc Listen to songs created by others
FROBITS