A song made by BanaT 2025
A song made by BanaT 2025
Mayo wandi Mary Lungu
Mayo zikomo kwambili
You guided me all the way
Mayo wandi
Mayo wandi Mary Lungu, munanipeleka mwambili
Tweze kuyenda kutali kusakila doti yo pangila nongo
Munanipuzisa kupanga nongo nakusigulisa
Mayo wandi Mary Lungu, munanipuzisa kulima milisi
Munanipuzisa kutwa sampo, anso futi sampo yamene noipanga unga
Mayo simwenze kugongo kuti ise tione chakudya
Eh, ayy, thank you Mayo
Mayo wandi, you showed me the way
Mayo wandi, every single day
Chikondi chanu ninyali yanga mwamene niyenda monse mofipa
Mayo zikomo kwambili, you lifted me higher
Mayo wandi Mary Lungu, my heart's true fire
Yoh, ayy, Mayo!
Bantu benze kuniseka kuti ba Mai bako nibosauka
Lelo ine neze kulimbikila kuyamika mbuye
Pali imwe mayo pantu simunakangiwe kunisunga
Namenje mukalikunisunga munjila zambili
Futi ukali kunisungila mwana
Mayo, you never let me fall
Mayo, you answered my call
Ayy, see this love oh!
Ba Tate banakusiyani, lelo imwe munapitiliza kunisunga
Mwezeli ba mai banga anso futi mwezeli ba Tate banga
Chifukwa munanipuzisa vonse mwamuna afunika kuziba
Muna nipunzisa kusunga ba kazi banga na bana banga
Munanipuzisa monkalila na bantu
Munanipuzisa kupasa ulemu bakulu
Mayo, you showed me strength
Mayo, you went to any length
Yoh!
Mayo wandi, you showed me the way
Mayo wandi, every single day
Chikondi chanu ninyali yanga mwamene niyenda monse mofipa
Mayo zikomo kwambili, you lifted me higher
Mayo wandi Mary Lungu, my heart's true fire
Ayy, Mayo!
Kulibe mukazi wamushe mutima monga imwe
Lyonse nimakumpempelelani kuli mulungu akazikusungani
Mayo, you are my strength
Mayo, you went the length
Ise nine mwana wanu, your last born Simon Kasonde Lungu
Nikuimbilani nyimbo yambili
Chikondi chanu chafuma mumutima
Mayo zikomo kwambili
Mayo wandi Mary Lungu muna nipunzisa njila yabwino
Chikondi chanu ninyali yanga mwamene niyenda monse mofipa
Nine mwana wanu, your last born Simon Kasonde Lungu
Nikuimbilani nyimbo
Mayo zikomo kwambili
Mayo zikomo kwambili
Mayo!
Mayo wandi Mary Lungu
Mayo zikomo kwambili
You showed me the way
Mayo wandi
Ayy, yoh, Mayo!
Thank you, Mayo
Mayo zikomo kwambili