Frobits
🎵 A song made on Frobits

Your Future Is Yours

0:000:00
Download
Reply with a song
Lyrics

Ana

inu…

mverani

bwino…

Kubadwira

m’

banja

lolemera,

sikutanthauza

kuti

mudzakhala

olemera.

Kubadwira

m’

banja

losauka,

sikutanthauza

kuti

mudzakhala

osauka.

Tsogolo

lanu

lili

m’

manja

mwanu…

Aliyense

ali

ndi

umoyo

wake…

Tiyeni… --- ##

[Verse 1] Ninaona

mnyamata,

anabadwira

m’

banja

lolemera,

nyumba

yabwino,

galimoto,

sukulu

yabwino.

Koma

anatsatira

anzake

oyipa,

mowa

ndi

mankhwala

osokoneza

bongo,

anasiya

sukulu.

Lero

ali

m’

misewu,

akupempha

ndalama,

chuma

cha

makolo

chatha,

dzina

lawonongeka.

Ninaonanso

mtsikana,

anabadwira

m’

nyumba

ya

matabwa,

amayi

ake

ankagulitsa

tomato.

Usiku

ankaphunzira

ndi

kandulo,

osataya

mtima.

Lero

ndi

namwino,

wamangira

makolo

ake

nyumba.

M’

banja

losauka…

mungatuluke

olemera. --- ##

[Pre-Chorus] Mverani

ana

inu…

Kulemera

kapena

kusauka

sizimasankha

tsogolo

lanu.

Tsogolo

lanu

lili

mwa

inu.

Gwirani

ntchito…

pempherani…

musataye

mtima. --- ## [

Chorus] **

Gwirani

ntchito

mwana

we!** **

Mulungu

akutsogolereni.** **

Mulungu

akutetezeni** **

ku

zinthu

zonse

zoononga

moyo.** **

Osasiya

sukulu,

ndiyo

kiyi

ya

tsogolo

lanu!** **

Osasiya

sukulu,

ndiyo

njira

ya

kupambana!** **

Tsogolo

la

m’

badwo

wanu

lili

mwa

inu.** **

M’

banja

losauka

mungatuluke

olemera.** **

M’

banja

lolemera

mungakhale

osauka.** **

Aliyense

ali

ndi

umoyo

wake…** **

Future

yanu

ili

m’

manja

mwanu.**

Musatsatire

anzanu

mwakhungu.

Akati, “

Tiyeni

tikamwe,”

kapena “

Tiyeni

tikabe,”

inu

nenani, “

Ayi!”

Mukudziwa

komwe

mukupita.

Maphunziro,

pemphero

ndi

ntchito

ndizo

zida

zanu.

Foni

yabwino

siimakupangani

munthu,

zovala

zamtengo

sizimakupangani

munthu.

Munthu

amadziwika

ndi

khalidwe

lake,

ndi

ntchito

yake,

ndi

Mulungu

wake.

Mwana

wanga…

dziko

lili

ndi

mayesero

ambiri.

Anzake

oyipa,

mowa,

mankhwala

osokoneza

bongo…

zonsezi

zimafuna

kuwononga

moyo

wako.

Koma

ngati

Mulungu

ali

nawe,

palibe

chingakugwetse.

Banja

lako

likuyang’

ana

iwe.

Dzina

la

banja

lako

lili

m’

manja

mwako.

Usalole

kuti

lithere

pa

iwe. **

Gwirani

ntchito

mwana

we!** **

Mulungu

akutsogolereni!** **

Mulungu

akutetezeni!** **

Pewani

anzake

oyipa,

pewani

zoipa

zonse.** **

Osasiya

sukulu,

ndiyo

kiyi

ya

tsogolo

lanu!** **

Osasiya

sukulu,

ndiyo

njira

ya

kupambana!** **

M’

banja

losauka

mungatuluke

olemera.** **

M’

banja

lolemera

mungakhale

osauka.** **

Aliyense

ali

ndi

umoyo

wake…** **

Future

yanu

ili

m’

manja

mwanu.** **

Gwirani

ntchito…

pempherani…

phunzirani…** **

musataye

mtima!** **

Gwirani

ntchito…

pempherani…

phunzirani…** **

musataye

mtima!**

Kubadwira

m’

banja

lolemera…

sikutanthauza

kuti

mudzakhala

olemera.

Kubadwira

m’

banja

losauka…

sikutanthauza

kuti

mudzakhala

osauka.

Tsogolo

lanu

lili

m’

manja

mwanu.

Pempherani…

phunzirani…

gwirani

ntchito…

Mulungu

akudalitseni

ana

anga.

Aliyense…

ali

ndi…

umoyo

wake…

Kachigamba

family

boys

susack

music

production

More songs by SUSACKprinters Listen to songs created by others
FROBITS