[male
vocals] (
Reggae
rhythm
kicks
in
with
a
steady
bassline)
Yesu,
yesu,
yesu.
Mundimvere,
Mbuye
wanga
Nkana
ine
ndimalakwa,
Koma
ndinu
moyo
wanga;
Mbuye,
mkhale
ndine.
Mbuye,
mkhale
ndine.
Mbuye,
mkhale
ndine
Mbuye,
mkhale
ndine
Ndine
mlendo
pansi
pano,
Msanditaye
m'dzanja
lanu,
Mundisunge
mwana
wanu;
Mbuye,
mkhale
ndine.
Mbuye,
mkhale
ndine.
Mbuye,
mkhale
ndine
Mbuye,
mkhale
ndine
Munafera
ine
kale
Kuti
mukandimasule,
Lero
lino
mndinyamule;
Mbuye,
mkhale
ndine.
Mbuye,
mkhale
ndine.
Mbuye,
mkhale
ndine
Mbuye,
mkhale
ndine
Mundidzze
ndi
chikondi,
Mndiyeretse
m'mtima
monse,
Chifuniro
change
mthyole;
Mbuye,
mkhale
ndine.
Mbuye,
mkhale
ndine.
Mbuye,
mkhale
ndine
Mbuye,
mkhale
ndine
Imfa
ikandifikira,
Inu
ndidzakangamira;
Ndikalowa
ine
m'mdima,
Mbuye,
mkhale
ndine.
Mbuye,
mkhale
ndine.
Mbuye,
mkhale
ndine
Mbuye,
mkhale
ndine
Yehova,
Mbusa
wangadi,
Ndilibe
kusowa;
Andigonetsa
bwinoli
Mumsipu
wokoma.
Cha
dzina
lakelo.
Ku
madzi
ake
odikha
Anditsogolera;
Ndi
moyo
wanga
wofoka
Aulimbikitsa.
Anditsogolera
m'njira
Zakulungamazo;
Chifukwa
changaay',
koma
Ku
madzi
ake
odikha
Anditsogolera;
Ndi
moyo
wanga
wofoka
Aulimbikitsa.
Ndipyola
kodi
chikhwawa
Cha
mthunzi
wa
imfa?
Ndilibe
mantha
ngati
'Nu
Mundiperekeza.
Ku
madzi
ake
odikha
Anditsogolera;
Ndi
moyo
wanga
wofoka
Aulimbikitsa.
Chakudya
changa
chabwino
Mwandikonzera
pha!
Pamaso
pa
adaniwo
Mudyetse
mtimanga.
Ku
madzi
ake
odikha
Anditsogolera;
Ndi
moyo
wanga
wofoka
Aulimbikitsa.
Mwadzoza
mutu
wanga
ndi
Mafuta
okoma,
Mwadzaza
chikho
changadi,
Inde,
chisefuka.
Ku
madzi
ake
odikha
Anditsogolera;
Ndi
moyo
wanga
wofoka
Aulimbikitsa.
Zokoma
ndi
zakuyanja
Zidzanditsatako;
Ndikhala
m'nyumba
ya
Mlungu
Ku
nthawi
zonsezo
Ku
madzi
ake
odikha
Anditsogolera;
Ndi
moyo
wanga
wofoka
Aulimbikitsa.
Inu
Mulungu,
tikuyamikani;
Tibvomereza
ndinu
Ambuyathu;
Ponse,
Atate,
akugwadirani,
Ndinu
wamuyaya!
Nanu
akukuzani
amithenga,
Nanu
zam’
mwamba
ndi
zamphamvu
zake,
Nanu
angelo
a
mitundu
yonse
Akuimbirani! “
Mbuye
Woyera!
E,
Woyera
nokha!
Mbuye
Woyera!
Mbuye
wa
makamu!
Ponse
ulemu
wanu
ndi
wodzaza
Pansi
ndi
Kumwamba.”
Nanu
Atumwi
akumveka
aja,
Ndi
Aneneri
oyanjana
omwe,
Ndi
aunyinji
anakuferani
Akuyamikani.
Mpingo
woyera
wa
kwa
anthu
onse
Ukumverani,
Mfumu
ndi
Atate,
Mwana
woona
wa
ulemu
wonse,
Mzimu
Nkhoswe
yemwe.
Kristu
Mfumuyo
yauleme
rero!
Mwana
wosatha
wa
Atate
ndinu!
Simunanyoza
mimba
ya
namwali
Potipulumutsa.
Imfa
mutagonjetsa
ndi
zowawa,
Njira
munatsegula
tikalowe
Momwe
mukhala
Inu
ndi
Atate
Mwaulemerero.
Kumva
milandu
yathu
mudzabwera
Mutithandize,
atumiki
anu;
Mwatiwombola
nawo
mwazi
wanu:
Mutipulumutse
Mtiwerengere
mMwamba
ndi
oyera;
Mutidalitse,
ndife
anthu
anu;
Moyo
wosatha
mutipatse
tonse,
Mutilamulire.
Tsiku
ndi
tsiku
timalemekeza;
Nanu
tikukuzani
osaleka;
Mbuye,
mtisunge
tingachimwe
lero:
Mtichitire
nsisi.
Mbuye,
chifundo
chanu
chitigwere
Monga
tikhulupira
Inu
nokha;
Ndakhulupira
zedi
mwanu,
Mbuye,
Ndisagome
konse! (
Fade
out
with
steady
bass
and
percussion)