[male
vocals] (
Soft,
melancholic
log
drum
melody
plays)
Yehova,
ndine
yani
kuti
mundikumbukire?
Mu
dzenje
la
imfa,
munanditulutsa
Chisomo
chanu
n'chachikulu
Ndikuyimba
za
dzanja
lanu
lachifundo
Ndinali
ku
ntchito
ndi
anzanga
makumi
asanu
Tonse
tinali
amuna,
tonse
tili
ndi
banja
Tinkagwira
ntchito
limodzi
mu
shade
Kuseka,
kuyimba,
ndife
abale
Tsiku
limenelo
ndinamva
kufuna
bafuti
Ndinati
dikhilani
ndinathamangira
ku
toilet
Sindingathe
kufotokoza
mmene
ndinamvera
Koma
mzimu
unandikakamiza
kukazithandiza
kutoileti
ya
andolo
Toilet
ya
ndolo
yandipulumutsa!
Machines
anaphulika
ine
ndinapulumuka!
Toilet
ya
ndolo
yandipulumutsa!
Toilet
ya
ndolo
yandipulumutsa!
Machines
anaphulika
ine
ndinapulumuka!
Toilet
ya
ndolo
yandipulumutsa!
Anzanga
onse
anamwalira
tsiku
limodzi
Koma
ine
ndinapulumuka
ndi
dzanja
la
Ambuye
Company
inawapatsa
ndalama,
azimai
a
ofedwawo
koma
moyo
sunabwerenso .
Ine
Ndinapita
kunyumba
kukauza
mkazi
wanga
Anayamba
kulira,
anayamba
kundimenya
Anati, "
kukonda
kutoileti
toilet
Mwandimanitsa
ndalama,
ndinadabwa
M,
Malo
mokondwa
ku
ine
ndilimoyo
koma
iye
nkumalila
ku
kukonda
toilet
ndalama
zapita
Zoona
ena
akazi
akhalira
cuma!
Mukazi
Wanga
anakakondwa
ine
kufa
iye
apatsidwe
ndalama!
Chikondi
can
mpeni
ku
mphatsa
Ndimayang'ana
kutsogolo
ndikuona
chifundo
Anthu
akufunsa
cuma
kopambana
moyo
wa
munthu
Palibe
chikondi
pa
make
ndi
ine
shuwa
Tsopano
ndikuyenda
ndi
mtima
wolemera
Kukumbukira
abale
anga
omwe
anapita
Ndimawapempherera,
ndikupempha
mtendere
Kwa
mabanja
awo
omwe
anatsala
Chisomo
cha
Mulungu
n'chakuya
ngati
nyanja
Chinandipeza
mu
nthawi
ya
chiwonongeko
Ndidzamtumikira
mpaka
tsiku
langa
lomaliza
Yehova,
ndine
wanu
mpaka
kalekale
Toilet
ya
ndolo
yandipulumutsa!
Machines
anaphulika
ine
ndinapulumuka!
Mukazi
Wanga
andidzudzula
akuti
bola
nkanafa
kuti
iye
Akhale
ndi
cuma
Toilet
ya
ndolo
yandipulumu!
Machines
anaphulika
ine
ndinapulumuka!
Thank
You
Jesus!
Nkama
ya
Mulungu!
Toilet
ya
ndolo
yandipulumutsa !
Zikomo
Ambuye,
zikomo... (
Fading
log
drum
and
soft
synths)