[male
vocals] (
Ayy,
yoh)
Iwe
Mavis,
wanditunza
mumtima
mwanga
Kuyambila 2018,
tili
pamo
mwanangu
Chukwu
alinaise,
akayankha
mapempelo
Mavis
wanga,
muli
shani
mama
Kuyambila 2018,
wanjikonda
boza
iyayi
Tikapitapo
mumavuto,
ma
stress
ya
chalo
Koma
chikondi
chathu,
chikala
ngati
lyon
Iwe
ndiwe
wanga,
sindikuweya
mwana
Ndiwe
chipangano,
chachikulu
pa
moyo
Odi
Mavis,
mune
wa
moyo
wanga
Chikondi
chathu,
nchamuyaya
Ngakhale
mwana
alibe,
Mulungu
alinaise
Atapasa
nthawi,
iye
azatidalisa
Mavis
wanga,
nkhala
wachimwemwe
Nthawi
zambili,
bantu
amakamba
Kuti
mwana
nchofunika,
koma
ine
Chikondi
chako
Mavis,
chija
chinkhala
Nidzafuna
iwe,
mpaka
mapeto
Fabian
Habusiwa,
wamukonda
m'bale
Natotela
kuli
Mulungu,
chifukwa
cha
iwe
Odi
Mavis,
mune
wa
moyo
wanga
Chikondi
chathu,
nchamuyaya
Ngakhale
mwana
alibe,
Mulungu
alinaise
Atapasa
nthawi,
iye
azatidalisa
Mavis
wanga,
nkhala
wachimwemwe
Mayo,
muli
mbali
yanga
Tikapilila,
kuli
mwayi
patsogolo
Mulungu
nsamala,
ifwe
tonse
Chikondi
chathu,
chidzakhala
champhamvu
Fabian
na
Mavis,
tili
pamo 2018
mpaka
lero,
chikondi
chiyaka
Natotela
Lord,
Amen
Natotela
Lord,
Amen (
Ayy,
yoh,
chikondi
chamuyaya)